Vi bøger
Levering: 1 - 2 hverdage

Mphaka Wamphamvu Zochiritsa - Tuula Pere - Bog

- Chicheva Edition of The Healer Cat

Bag om Mphaka Wamphamvu Zochiritsa

Celesse, the healer cat, is a highly respected member of the neighborhood. As the mistress's favorite cat, she spends lazy days in the warmth of the house. One snowy night a mother hare rushes in, desperate for help. Reluctantly, the healer cat travels with her through a nighttime snowstorm and biting cold winds. In a dark forest, Celesse comes face-to-face with a scary surprise and is forced to gather her powers for the first time in a while. --- Mphaka winawake dzina lake Silese, ankatha kuchiritsa matenda osiyanasiyana. Chifukwa cha mphatso yakeyi, mphakayu ankalemekezedwa kwambiri m'dera lonse limene amakhala. Nawonso adona a m'nyumba imene Silese ankakhala ankam'konda kwambiri poyerekeza ndi ziweto zonse zimene anali nazo panyumbapo. Tsiku lina, mwana wa kalulu anadwala mwakayakaya. Mayi wake ataona kukula kwa matendawo, anapita kukapempha mphaka wochiritsa uja kuti abwere adzathandize mwanayo. Koma mphakayo sankafuna kumuthandiza chifukwa kunja kunali kutada komanso kukuzizira kwambiri. Kaluluyo ataumirirabe, mphakayo analolera n'kunyamuka. Ali m'njira, anakumana ndi nkhandwe yoopsa kwambiri. Koma Silese anakwanitsa kulimbana nayo ndipo anapitiriza ulendo wawo. Kenako anafika kunyumba kwa kaluluyo ndipo anathandiza mwana wodwala uja. Kutacha m'mawa, dzuwa linatuluka ndipo kunja kunayamba kufunda. Silese anauyamba ulendo wobwerera kwawo ali ndi chimwemwe chodzadza tsaya.

Vis mere
  • Sprog:
  • Ukendt
  • ISBN:
  • 9789523571600
  • Indbinding:
  • Hardback
  • Sideantal:
  • 40
  • Udgivet:
  • 21. Juli 2019
  • Størrelse:
  • 254x203x6 mm.
  • Vægt:
  • 363 g.
  • 8-11 hverdage.
  • 15. Oktober 2024

Normalpris

Medlemspris

Prøv i 30 dage for 45 kr.
Herefter fra 79 kr./md. Ingen binding.

Beskrivelse af Mphaka Wamphamvu Zochiritsa

Celesse, the healer cat, is a highly respected member of the neighborhood. As the mistress's favorite cat, she spends lazy days in the warmth of the house. One snowy night a mother hare rushes in, desperate for help. Reluctantly, the healer cat travels with her through a nighttime snowstorm and biting cold winds. In a dark forest, Celesse comes face-to-face with a scary surprise and is forced to gather her powers for the first time in a while. --- Mphaka winawake dzina lake Silese, ankatha kuchiritsa matenda osiyanasiyana. Chifukwa cha mphatso yakeyi, mphakayu ankalemekezedwa kwambiri m'dera lonse limene amakhala. Nawonso adona a m'nyumba imene Silese ankakhala ankam'konda kwambiri poyerekeza ndi ziweto zonse zimene anali nazo panyumbapo. Tsiku lina, mwana wa kalulu anadwala mwakayakaya. Mayi wake ataona kukula kwa matendawo, anapita kukapempha mphaka wochiritsa uja kuti abwere adzathandize mwanayo. Koma mphakayo sankafuna kumuthandiza chifukwa kunja kunali kutada komanso kukuzizira kwambiri. Kaluluyo ataumirirabe, mphakayo analolera n'kunyamuka. Ali m'njira, anakumana ndi nkhandwe yoopsa kwambiri. Koma Silese anakwanitsa kulimbana nayo ndipo anapitiriza ulendo wawo. Kenako anafika kunyumba kwa kaluluyo ndipo anathandiza mwana wodwala uja. Kutacha m'mawa, dzuwa linatuluka ndipo kunja kunayamba kufunda. Silese anauyamba ulendo wobwerera kwawo ali ndi chimwemwe chodzadza tsaya.

Brugerbedømmelser af Mphaka Wamphamvu Zochiritsa

Find lignende bøger
Bogen Mphaka Wamphamvu Zochiritsa findes i følgende kategorier:

Gør som tusindvis af andre bogelskere

Tilmeld dig nyhedsbrevet og få gode tilbud og inspiration til din næste læsning.